Scandal News
Blantyre, Malawi
|
May 30, 2025
Sad Story of My Wife; Mother of Our Kids
Chapter 3: MY WIFE & MOTHER OF OUR 3 KIDS ,TELLS ME I DON’T SATISFY HER SEXUALLY AFTER BEEN TOGETHER FOR CLOSE TO 13 YEARS. Ndikufuna kuti ineyo ndikhale bambo woyamba to come out and speak out inner feelings, pains, abuses and experiences encountered in intimacy relations and/or marriage. Amunafe we were groomed never to shed a tear. Takhala tikhuphuzitsidwa kuti Mamuna salira amangosisima basi. Takhala tikunamizidwa kuti mamuna asamayakhule zakukhosi olo nkhaza zomwe amakumana nazo mubanja chifukwa aziwoneka ngati wofowoka komaso wopepela and wopusa. Zimenezi zapangitsa azibambo komaso achinyamata ambili to commit suicide. Currently mu suicide deaths statistics of 2024 in Malawi zinawonesa kuti Azibambo anatsogola ndi 80% kuposa 20% ya azimayi ndi asungwana omwe anazipha. #DISCLAIMER : Post iyiyi sinalembedwe kuti iyipitse mbiri ya munthu olo kufuna kufalitsa UMTHENGA WABODZA. Ndikulemba as munthu wokhudzidwa komaso in good faith to enlighten fellow men in similar situation like mine and others to learn and Garner courage to stand up to overcome depression and temptation to commit suicide. This is in utmost interest of national importance as we are advocating for Mental health and awareness. Why am highlighting my divorce on Facebook,is because nthawi yomwe tikapanga ukwati ndinapangaso announce pa Facebook on 17th August,2018(see screenshot attached). So pangoyenela kutelo. •Banja lathu tinadalitsa pa 8 September,2018 koma tidali titakhala pachibwenzi kwa zaka folo (almost 4 years). Ine ndi Ma Achisomo,both of us we are in our second Marriages, respectively. •Banja langa linatha because I personally divorced my former wife because ndikafuna kukwatila Ma Achisomo. It was Consensual Divorce. Banja la Ma Achisomo silinathe, anasiyana ndi mamuna (MHRIP) wawo chifukwa cha imfa. Ndipo imfa yake ndi ya suicide. Anachita kuzipha yekha poziponyela pa sitima. Chomwe anandifotokozela Ma Achisomo ine ndi chakuti , zifukwa zake zinali za mavuto abanja mwawo. Ma Achisomo anakhala pa banja kwa zaka eyithi koma opanda mphatso ya mwana. We met around 5 – 6 months after burying her husband. The first day in her house in Steenberg, Capetown South Africa ( was a wendy house nyumba Yama tabwa- picture attached) tsiku lomwelo tinakazinga chipisi. Kuchokela pamenepo kwa two months timapanga tsiku lililonse. Either abwela kwathu ku Kensington olo ine kupita kwawo. Then she got pregnant (ndinapatsa mimba). We went to Discherm and they confirmed yes she conceived and expecting a child. Unfortunately, we couldn’t keep the baby as anali asanasuzilidwe kupanga allowed to stop wearing black cloth and chiliza anali asanamange. So if she were to keep the pregnancy pezi after 1 year ,ikuwonekela. Ndiye sizinakawoneka bwino kuchimuna kapena zinakatha kupeleka maganizo olakwikwa. So mimba inachotsedwa ku chipatala chaku Belleville. After been set free, we courted for a year and few months. Then I moved in her house kuchoka kunyumba kwanga cholinga kuti tiziseva ma expenses, so we stayed in marriage by cohabitation for a year and few months then she got pregnant again. After 3 months we officially got married In 2019 and I bought a piece of plot in Malawi and started building, she resigned from her work when she was 5 months pregnant, kenako our first child was born. Fast forward to 2020. I resigned from work to start my online business , then I came to Malawi to supervise 🏠 construction and as well register my company on 29th October,2020. I later participated several procurement events. I was awarded my first contract in January,2021. I delivered and was paid K2,500,000. And, someone gifted me K2,500,000, total K5,000,000. I went back to Capetown and told my wife we are coming back to malawi by faith. Zochitika zikawoneka konko. After the birth of our child, we were having issues in our bedroom as she begun to deny me citing post traumatic pregnancy issues, as well fatigue komaso loss of libido due to contraceptives. I had to invite a senior married couple to counsel us on intimacy issue. This happened in Capetown not Lilongwe. Titabwela kumalawi ndiye ma excuses left and right. Pena kumangokhala nyumba ngati chimwene ndi sister wache. Pena zimatheka mokakha paka ana awili kubadwa. Nthawi zambili Ma Achisomo amati akutopa chifukwa ntchito za pakhomo. Then I decided to employ 3 maids (see attached advertisement,ndinafunsa pa Facebook popano kuti ndikufuna nanny) azimayi antchito atatu,each was paying K65,000. Cholinga changa ndimafuna iwowo asamagwilie ntchito ina iliyonse azingopanga supervise and kupuma basi. Cholinga ndikabwela ku ntchito ndikawafuna kuchipinda asamati atopa. Koma zimakanikabe it’s headache,gas olo maperiod olo chamimba olo kutopa olo sali mood. From 2023 -2024 – timangokhala no kiss,no any form of intimacy. Olo hagi amakana. Olo kuwamenya nthako amadana nazo. This period mwina ngati tinagonanapo sikangapitilire ka 10 in two years. KOMASO kugonana kwake kokuti ndawakakamiza komaso yeyo kungoti bwela umalize. While kuchipinda zikuvuta,mbali mu akundiyakhula mwamwano pamaso pa anthu antchito,ana anga komaso mokuwa mokuti kuno ku Airwing,ma nebas anga onse amadziwa ndine chitsilu chododedwa ndi zimayi because kunyozedwa,kupepesidwa, kutukwanidwa zakabudulu ndi kwa daily. I tried booking nights at hotels kuwatenga kuti mwina tichenje environment zimakanikabe. I have taken her 6 times on my international business trips. Kupita kunja koma sekisi kumandikanabe olo kupanga moti sakufuna kungogona chagada,nkhope itayang’ana kumbali. I endured everything from 2023 to 2024. Around october of 2024. I was extremely depressed. By this time zinandikwana pamaso pa anthu I was trying my level best to give a good picture of my marriage. I used every time celebrate her on this page. Kuchemelera,kumuyamikila pazabwino zomwe ndimawona pa iye. Koma yeyo on her page samandipanga post olo kundiyamikila. It was only me kupanga post. She randomly posted me on my birthday or our marriage anniversary. Ndikafunsa amati alibe nthawi yopanga post. Ndimasowa kuti nkhaniyi ndikamuwuza ndani, sandiseka,sindiwoneka ngati chitsilu kwa azizanga. In November ndinagula tameki kuti ndiziphe. I don’t know how God rescued koma pezi pano mukuti Yamikani Nicholas Kachingwe anazipha KOMASO mwina pezi mukuti ndizipha kamba kangongole osati nkhani zabanja. I gathered courage to inform my mother in law and my only sister who serves as a mother in our family. Both of them samakhupilira kuti I have endured for two years in a loveless, sexless marriage. And, they blamed me for keeping it inside me. Anati problem shared is half solved. This is in 2024 around November and December, here is what followed; Both of them spoke with her. Ma Achisomo anamasuka kwa mai awo in their family WhatsApp group through voicenotes,anati :” ine Bambo Achisomo ndilibe nawo mafeelings,komaso sindifuna andiwigile thupi langali,amandinyasa ,he makes me comfortable , in short ndilibe nawo chilako lako china chilichonse.” Koma yeyo anaphatikiza ndi nkhani yoti ndinapasa makofi chifukwa chopepha ndalama kwa azimuna okwatila pamene yeyo ali kanzi wamwini komaso ali multi-millionaire payekha ( I will explain in Chapter 4 why Ma Achisomo is a Multi-millionaire). KOMASO MAI ACHISOMO AMANDILIPILITSA KUTI NDIGONE NAWO. NDIKAWALIPILA AMANDIPATSA YONSE NDINGAFUNE NDIKAKANA AMAKANA. I EVEN WROTE A POST ON FACEBOOK ABOUT IT. SEE SCREENSHOT. Apongozi anga anamuzuzula kumuwuzeso kuti akusambila manja l, banja lake likatha zikhala zofuna zache. Ma voicenotes alipo both amai Achisomo KOMASO Apongozi anga. I will release them another day. Mai Achisomo zimawavuta kukhala bwino ndi azimayi antchito. Amayakhula mokhazula komaso mwamwano,amafuna kugwadwilidwa ngati Mfumukadzi. Ali ndi katima ka umbombo. Kuwelenga nthuli muphika, kuwelenga ma slice a bread. Amalorela zakudya kuwola mu fridge than kupatsa watchito. Zonsezi Azimayi antchito opitilira 10 alipo ndipo they gave their testimony in recorded voicenotes. Ndiye amafuna kuti ineyo azindituma kukakalipila antchito akatenga mutu wa nkhuku wawo omwe iwo amawukonda olo akatenga chiboda olo akamwa sobo olo kudya nthotchi olo akalikwisa china chilichonse. So ine ndimakana kuti chonde musandikhuzitse zinthu zaku kitchen. Am a man zimenezo ndi za azimayi. Vuto lina,Mai Achisomo anadya matako agalu satha kukhala pankhomo. Amangokhalira kuyenda especially pomwe ndinawapasa boutique shop. Amachoka 8am kufika 7pm from Monday to Friday. Our last baby,amamwa S26 gold. So ndinawawuza they should give me notice two days in advance asanathe because kakawo ndiwodula, sindikuyenela kupanga budget. Tsiku lina, nanny wina zina lake Mwiza. Mwiza amapanga kaka wamasana whilst Mai Achisomo amapanga wa utsiku wogonela. It happened kuti iwowo abwela utsiku. Then anapeza kuti kaka watha sufika mamawa. Anayamba kumulalatila tsikana uja ati: Ma Achisomo: Bwanji sunawone kuti kaka ukutha kapena kunena? Mwiza: Pepani,lero tidali bize komaso mesa inuyo mumapangilaso utsiku ndiye ndimaganiza kuti mukuziwa? Ma Achisomo: Za manyi zimenezo. Ndi udindo wanga owona zomwe zatha nyumba muno,zopusa ndimadana nazo. Mukufuna mundikalipitse kwa Bambo Achisomo? Mai Achisomo anatenga chitini cha empty cha S26 Gold ndikugenda nacho nanny uja. Nanny came to me panja angolira. I went to Mai Achisomo and told her nonse munalakwisa,komaso inuyo Mai Achisomo nyumba ino ndi yanu osati atsikana antchito. Why iwowo azikhala bize kuyendetsa nyumba yako. Because umangokhalira kuyenda yenda that’s why pano ukulephela kuziwa zomwe zikuchitika nyumba mwako. See three WhatsApp Conversation Screenshots attached.Mai Achisomo sent those messages to me and these were her words; ” Ndiwe Mamuna Wopusa, Chitsiru,wozaza mamina mutu, Chitsiru cha Munthu,I will never forgive you for supporting ma nannies over me, ndipo USAZANDIGWILESO NTHUP LANGALI NGATI ZINGA KUWAWE YOU CAN DIVORCE ME.” She went further to add:”MAMUNA WOPUSA NGATI IWE SINDINGAMUTSEGULIRE MIYENDO, IDIOT,BOLASO NGATI UMAFIKILAKOSO,Mxii.”I asked , ngati ndimafikila kutiko? She never responded. In short what she meant is; after giving her 3 kids,after loving her and living with her for 12 years, she has realized I don’t satisfy her sexually. In other words it means there was or there is someone who is better than me in bed. Zimenezi zimandisowetsa Mtendele. I consulted a legal advisor and to commence divorce filing. But my biological father stopped me and said I should give my Marriage another chance , the issue we kept with close family members. I cancelled the divorce submission. We then went to Tanzania together (picture attached) for the very first time in two years we had the best intimacy and sexual relations as a husband and wife right there. And, everything went well. Then in January,2025 ndipomwe amapephetsa ndalama kwa mamuna wapabanja,ati amafuna Fanta ndi KFC komaso kundinyoza yet ndapanga sponsor trip yopita kutanzania just few weeks ago. Fast forward to March – April. I bought a piece of land for my daughter Chimwemwe. Something evil and disappointing occurred( will explain in Chapter 10) that led me to re-open my divorce case and file it. So ,yes I filed for Divorce because My wife of 13 years anandiwuza kuti I make her uncomfortable ndimakagwila mabele olo kuyamwa ma titties ake komaso ati alibe nane mafeelings komaso amandikana kuchipinda. Pokha,pokha ndilipile ndipomwe angandipatse yonse NDINGAFUNE. Zimenezi amawawuzaso atsikana antchito kuti ine Bambo Achisomo ndimawalipilitsa. Ineyo was just pampering her I didn’t know kuti amazitengela serious. Yes so ,the reason I divorced her is: SHE ABANDONED HER SPOUSAL DUTIES AND INTIMACY DESERTATION, DENIAL OF INTIMACY. #Conclusion Pali anthu ena amati,iwe Yamikani think about the kids.Kodi inuyo zomwe mwawelenga mwambamo. Why the mother of three kids analibe nazo ntchito kuti banja lake litha kutha. Why are you interested to reserve her respect pomwe mwina wakeyo alibe nazo ntchito ngakhale ali Mai wa Dorica. This is the reason why I stopped going to Church.So many hypocrites.She never missed church service koma yet pankhomo akunditukwana “Machende ako,Pantumbo pako.”Kodi what if I didn’t speak out last year ndikuzipha. Ndiye kuti munakasangalala?Why do we rush to judge munthu when he is crying out for help? Do you know the reason I announce my Divorce publicly? She challenged me kuti: “Stop stalking me,why are you obsessed with me mesa wati sukundifuna? Fulumila ndi Divorce yakoyo, Amuna Azako Anzeru anditole.” That’s when I realized Mai Achisomo never loved me. She used me to heal during her mourning period. She stayed with me coz I made her pregnant komaso I had potential to become a millionaire. She later got millions from me and become independent financially. Ndipamene nthupi lake linayamba kundikana automatically because she never loved me, that’s why amanyasidwa ndikamugwila because thupi limakana linatop kupanga pretend. So these 13 years it was just a lie. MY FORMER WIFE NEVER LOVED ME THAT’S WHY AMATHA KUNDITUKWANA ZAKABUDULA KOMASO KUNDIPEPUSA KWA MA EX-BOYFRIEND AKE. Can you imagine Ma Achisomo amalumbila ka folo bayibulo manja uku akulira kuti sanandipangepo cheat olo kucheza ndi EX-BOYFRIEND mosefukila. Lero ndi izi. Mfiti yayikazi ndiyowopsyatu. So ndinayika pa fesibuku za divorce zo kuti Amuna anzeruwo adziwe kuti ine ndathana ndi Mai Achisomo atha kuwakwatila. Why am I publishing these Chapters is because I want my fellow Men to gather courage and to to know it’s okay to speak out. It’s okay to cry. It’s okay to say am abused by my wife. Abuse is not only violence. Emotional,Verbal, Sexual, Financial and Denial Of Marital Intimacy can also be deemed as abuses. Tsono mumakayakhula mu mapage mwanumo pofuna mafollowers please do share facts awa. Ine sindili muchigoba. Ine I don’t cut corners. I speak live and direct. Kodi mumafuna ndiziphe ngati mamuna zanga uja? I refused to commit suicide. I chose to stand up and fight for my freedom. I chose to walk away from An abusive, Manipulative,Toxic, Narcissistic, Loveless, Sexless, Joyless and Hypocritical Marriage. A sham of Marriage. Never again. I don’t care if you want to call me a COWARD OR WEAK. Am owning my Truth. Am writing my own true life story. I have my pen and paper. I shall share everything I endured in my marriage of 1e years. Ena kumafunsa kuti kodi palibe zabwino zomwe Mai Achisomo amapanga. Muwelenge zomwe ndakhala ndikulemba pa page pano for the past 7 years about her. Ine sindisiya until Chapter 20. Dziko lonse lidziwe china chilichonse kuti Ndizotheka komaso zikuchitika mamuna kuzuzidwa mu banja ndipo is possible for a MAN TO SPEAK OUT WITHOUT FEAR OF BEING CALLED A COWARD. LOADING 👇. Chapter 4: HOW I EMPOWERED MY WIFE TO BECOME A MILLIONAIRES AND SELF RELIANT BUSINESS WOMAN.
Read more
Blantyre, Malawi
|
May 29, 2025
Chapter 2: Why did I Slapped My EX-Wife
Inetu sindibasala kuseli kwa Pemphero Mphande . Kutumiza post as anon. No. Ine ndimalemba in my name on my page because everything is true and I have the receipts. Sindikamba zinthu zopanda umboni. Ndilibe nthawi yonama olo kunena miseche olo mabodza. Why, am doing this? is BECAUSE I LOVED HER,I STILL LOVE HER BUT SHE REALLY HURT ME AND UNTIL NOW SHE HAS NO REMORSE. I built my future and everything around her but she BETRAYED and BACKSTABBED me IN SECRET and am here to reveal everything publicly for my closure and healing process. I need to speak out now not tomorrow. Last year somewhere in November or December, I booked a marriage counseling session with Rev Yasin Gama of Mvama CCAP. That day our car went for maintenance and we hired a private taxi with a driver. During the trip, I was on a call , Ma Chisomo asked me for Airtel money of K1,500.00 (one thousand five hundred kwacha) while I was still speaking on the phone and ignored her. After I finished my call. I asked her, kuti bwanji sumawona ndinali pa call komaso why asking K1,500 ya data yet you have K25,000 ku account yako ya Airtel money. She responded: ” Aahh inu, 1,500 yomweyi kuchita kuyakha choncho, Kodi mesa mumati ndinu bwana.” Ine I responded ” the issue is not the amount koma mene wapemphelamo after all iweyo tili ku Capetown unayambapo wandigulira Airtime ya R10 or kumalawi kuno ya 500 Kwacha. Please use your money, don’t bother me. I won’t give you” Kenako yeyo said,” ndiye chifukwa chani umandiletsa kukapempha ndalama kwa amuna ena?.”I remained quite. Nkhani yomuletsa kupempha pempha is like this; 1) Mfumu Kapingama this is one of my close friends, he is in America now. Last year Ma chisomo commented on his Facebook page kuti “mula tigayileniko ya fanta, malawi wavuta.” George said nditumiza mula. It ended there. I saw her comment but I ignored it as just for jokes. Second time she commented on another post reminding him to send the money. That day, I cautioned her Kodi bwanji ur embarrassing me publicly komaso kwa azizanga. Iweyo you have a shop and millions, even today you can buy more than 50.crates of fanta pawekha. Why are you doing this? She apologized. I forgave her. 2) pali tsikana wina wake amati Aggie wa kappa, they only know each other through my page. Anamupepha tsikanayu kuti amugulire Nivea ku Sasafulika. And, the lady bought it. Then cautioned her again kuti why kupephapepha as if I can’t provide olo iweyo sungagule wekha? 3) Blessings also known as ALONGOSI based in Capetown: Tsiku lina tili kumunda, ALONGOSI is her male best friend amayakhulana pa week may be more than 5 times. He called and she told him tili kumunda kuzathila fertilizer. ALONGOSI anayakha nanetu pano ndakolola 50 bags ya maize. Ma Achisomo anapepha zawoyo and he responded mkazi wa Bwana ngati iwe uzipepha chimanga. I told him he should ignore it. She is just joking. I asked her kuti Mai Achisomo are you trying to say ifewo we can’t afford to buy chimanga kuti iweyo uzipephetsa kwa zako wamuna anapepesa. Tinafika Kwa Rev Gama. We did first session then we were meant to go for two sessions as well. He asked us to discuss when we reach home when to do it. Tinafika kunyumba utsiku. I asked her when should we go. She responded ine sizapitakoso iweyo umawawuze zonse abusa aja instead of kungoyakhula zazing’ono. So I don’t want counseling anymore. I asked why did she say “ndiye bwanji umandiletsa kukapepha kwa amuna ena” do you think ndi mau abwino. Amayakha mwano then I slapped her twice. Yeyo anatenga chi brush cha kutoilet kundimenya then she wanted to take mirror ya ku toilet kuti andiswele mutu. I locked her in the toilet and asked the maids to open the door after 10 minutes after she calms down. I forgot my phone in the toilet anayimenyetsa pansi four times koma sina sweke then kenako anatenga zovala zanga kuzidula dula. (Video is below.) I did apologized to her, mother inlaw, her sister and my sisters that yes what I did was wrong to slap her. And, this was once in 13 years we have been together. Mind you. All this while I was still celebrating her and taking her along to my international business trips.
Read more
Blantyre, Malawi
|
May 28, 2025
Chapter 1: My 2025 Divorce – Did My Wife Cheat on me?
I must say outright, I have no substantiating evidence alleging an infidelity. I only have suspicious incidents. Ndikuti ndilibe umboni wina uliwonse ogwilika oti Mai a Chisomo CHEATED on me. Ngakhale zili chonchi panali zina ndi zina zimandisowetsa Mtendele komaso kundipatsa maganizo. That’s why I did not divorce her based on adultery grounds. I have no evidence kuti anapanga chigololo olo ali ndi chibwezi kapena anali ndi chibwezi. #FirstIncident: The screenshot attached below was captured on 10th January,2025 on Friday at 11:23pm. Nthawi imeneyi ndinali ndili panja ndimapanga zina ndi zina or either I was smoking not knowing Mkazi wanga akucheza ndi EX wake. I found her asleep. Wanted to do check something in her phone ku WhatsApp, I usually send my important information to her to record and keep on my behalf. Ndipamene ndinapeza nambala ya ex wakeyu amene zina lake lili Leesto Phiri , they were in online committed intimate relationship around 2010 to 2013. Unfortunately their WhatsApp conversation was deleted but she forget to delete the name. That’s how I found it. I just took the below screenshot and, there was a sensitive video as well in her gallery. I confronted her same time, she said uyoyo “LISTO was asking her about prices of work suits and safety boots.” I quizzed her why didn’t contact me directly and if it was an honest conversation why did she deleted it. And, she said the video was her personal thing as she was checking something like a pimple or something. Kenako anayamba kulusa why touching my phone, do I touch yours? Bwanji ukundipanga stalk. She said I have insecurities and low self esteem. I left the conversation at it. I realized they’re Facebook friends whilst ine ndikawona ngati anabulokana. It really irritated me when I discovered that she went even far by liking his wife’s picture (see attached and name showing “Ma Chisomo”). Why liking the picture of your Ex boyfriend’s wife? #Second Incident From her own mouth she told me , kale kale in early 2000’s Happy (name withheld) used to go out with her friend and then best friend of his was Phiri (name withheld). Phiri yo amkafuna Yamie koma Yamikani amamukana. Even Yamieyo aunt ake told her kuti amulore adye dolla koma Yamie amakana. Fast forward to 2025. At Airwing, there is mechanic specializing in Germany cars – benz, Volvo, VW etc…. Phiri and Yamie met there. Yamie was going to Gateway Mall. Phiri left his car at the garage and asked for a lift from Yamie. Yamie was with her Niece Yankho. They did give him a lift. This incident anandiwuza yekha Yamikani yo. Amvekele; “ndafuna kukuwuzani izizi mwina anthu ena atha kubwela olo utha kumva kwa ena and ziwoneka zina zake. Ndinakumana ndi Abwana ako akale a Phiri ndipo ndawapasa lift koma Phiri yo amakuwopa iweyo kuti ukamuwona mu galimoto ali ndi ine utukwana komaso umuyalusa pa fesibuku. Koma ine I told him Yami is not like that and Phiri to told me to tell you kuti usazapangenso zandale just concentrate on business.” Imagine. Ndinangomwela madzi koma mumtima mwanga munali mafunso opanda mayakho. #thirdincident Sometime back coming from Tanzania, during transit at Chileka Airport. We were sitting pa mipando yokhala athu atatu. She received a phone call from a man and they chatted I enquired from her ndi ndani after the call she told me “it’s her ex boyfriend waku Ndirande akuti amapatsa moni.” I shouted at her mu ndege momo kuti zowona ur talking to your ex boyfriend in front of me like seriously. Even neba wathu pa mpando looked at me and gave me a sign to calm down and resolve the issue at home not publicly. I remained quite didn’t speak to her all the way . When we landed in Lilongwe. She told me she has blocked the guy. #Conclusion. These are only suspicious incidents I have come through, though palibe umboni ogwilika opanga cheat. Only God knows. That’s why this is not the reason why I DIVORCE HER. For clarifying and control: For 8 years. I have never cheated on my wife. I have never fucked any woman in these 8 years. There is any woman I have slept with from 2017 to 2025 apart from my wife. FEEL FREE TO COME OUT AND EXPOSE. Am committed man. Am loyal and faithful. Am challenging ngati alipo tsikana wina aliyense ndinanyengana naye from 2017 to 2025 in May. Bwelani muzanditsuse. Sikuti ma temptations sindimakhala nawotu. Analipo ambili I could have also cheated bobo koma ndimazibweza kuti no . I made vows. I will break any vow. This is my way of healing. Pakali pano sindikupanga za ulemu or za maturity. Ndilibe nazo ntchito.hese issues were burning in my heart. I have to let them go to. Zikomo.
Read more
Washington State,
|
May 27, 2025
The Myth About Penis Captivus – Penis Trapped in the Vagina
In Malawi just like other African countries, there is a strong belief in the power of Juju in almost every sphere of life, be it soccer, wealth including romance among others. Most people believe it is possible to put a spell on your spouse so that he or she gets stuck in the process making love. Many people who travel to South Africa to seek for greener pasture are usually believed to use this kind of juju to ‘Lock their wives“. However, contrary to this belief, medical studies conducted on this matter have established that this is a rare condition where a man’s penis becomes trapped within the vagina due to vaginal muscle spasms called “Penis captivus,” also known as “Genital Incarceration. While it sounds like a myth, it is a real, albeit extremely uncommon, phenomenon. The most frequent cause is vaginismus, where the pelvic floor muscles involuntarily contract, narrowing the vaginal opening and preventing the penis from being withdrawn. This is usually observed when dogs are mating, they get locked. Anxiety disorders, childbirth injuries, and prior surgery are some of the factors that cause Vaginismus for Penis Captivus. Vaginismus can make activities like inserting tampons difficult, and it can also interrupt penetrative sex or make it uncomfortable. Just because many people do not understand the causes of Penis Captivus is is regarded as either a myth often discussed in a humorous light. Reports of penis captivus have been documented in medical literature, including an 1884 case published in The Philadelphia Medical News and later found to be a hoax by Sir William Osler. In some cases chloroform has been used to relax the muscles and release the penis as treatment. The condition is considered rare, with only a handful of reported cases in medical literature. Witch doctors have taken credit on this issue because it is widely believed that it is the power of juju that causes this to happen. So next time you come across an incident of Penis Captivus, just rule out the possibility of Juju being involved.
Read more
Lilongwe, Malawi
|
May 24, 2025
Seven Arrested for Immigration Crimes; Released Under Suspicious Circumstances
Department of Immigration in Lilongwe on Thursday arrested 7 Malawians who had wanted to obtain Service Passports to travel to United States for work. The names of the suspects are Mr. Madalitso Kapangazina, Mrs. Maria Chimana, Ms. Sarah Nanthoka, Mr. Stain Ethics Mabere, Chinsisi Richard Phiri, Thandi Aresandra Phiri and Zaithwa Boston Kamanga. The suspects used fake letters from Ministry of Trade and Industry as well as Ministry of Agriculture. The letters indicated them as Directors in these respective ministries. The suspects were taken to Lilongwe Police where they spent a night. Meanwhile, today while Immigration were prepared to take them to court, they received calls from top Government and MCP officials to release them with immediate effect. They have all been released as it is believed that this is masterminded by a party loyalist officers.
Read more